On Saturday, May 10, 2025, Waxy Kay released his new single “Mumba” with Kinta on his Official YouTube channel. Whether you are a fan of Waxy and Kinta or just simply someone looking for meaningful lyrics, this song is bound to leave an impression. Its irresistible music and unforgettable, mindblowing lyrics make it impossible not to sing along. Read Mumba lyrics by Waxy Kay and Kinta below and experience the song’s passion.
Song Credits
Sone Name | Mumba |
Lead Vocals | Waxy Kay & Kinta |
Song Writer | Waxy Kay & Kinta |
Music Producer | [?] |
Label | Waxy Kay |
Release Date | May 10, 2025 |
Song Language | English |
Copyright © | Waxy Kay |
Lyrics of Mumba by Waxy Kay & Kinta
Waxy Kay
Kinta
Yeah
Mukanganilana Hip Hop Yangayo
Yeah Ti Ma Rappers Tina
Ndinkasiya Martse Adye
Tina Tinadyedwa Tina
Tungoyimba Masanje
Umva Hip Hop Ili Kuno Eeh
Hip Hop Ili Kuno
Pamene Olo Hip Hop
Sanayiwoneko Or Mphuno
Zi Ma Rappers Za Sober Zi
Ma Rappers Za No Nazi
Zosadya Beef Koma Zi
Aswisili Zononazi
Pa Ground Zili Poor Za
Phokoso Pa Media
International Level Yawo
Yungothera Namibia
Sangatsutse, Sangadziwe Or Jay-z
Kuti Anthu Awatchule
Alembetse Dzina Pa Jersey
Nti Ma Fame Tawo
Tongopindula Ma Babe
Muzalira Tikazatha Kasakeni Ma Veip
Of Course Malami Ndiwa Ng’ono
Koma Ife Anatilola Kwa
Inu Ananena No-no
Olo Inu Mu Top 1 Million Inu Mulibemo
Mu Trouser Mwanoumo
Momwe Muli Luso
(Kape Iwe Eti)
Mukufunika Tsache Ndi Broom
Azam, U-fresh Ndi Boom
Tikumane Tikhale Nkati Mu
Ti Clean Hip Hop Nkatimu
Kapena Tiitane Mumba (Eeeh)
Kapena Tiitane Mumba (Iwee)
Kapena Tiitane Mumba (Eeeh)
Kapena Tiitane Mumba (Haha)
Ukakawona Ka Waxy
Mphwanga Ukapewe
Ati Ukufalitsa Ndiwe
Mfumu Kape Iwe
Pamene Timalimba Ife Iwe Sungafewe
Simunga Rung Game Yi
Chokani Ana Amatewe
Ma Empty Tins Ofunika
Kuwathira Phuzo
Nyimbo Zawo Zilibe Bwanji
Akaphunzire Judo
Mukakhuta Kachasu Mic
Sipophwetsera Nkuto
I Drive You Crazy Or Muli Pa Neutral
(Malo Omwera Mowa Kuno Kulibe)
Eya Waxy Wagetsa Zi Ma Bars
(Hater Sakumwa Nawo Tea Olo Madzi)
Eya Waxy Wagetsa Zi Ma Bans
(A Tangoblower Ena Sizikuwayendera)
Wayika Road Brock
Wayimitsa Zi Ma Bus
Koma Tu Ankandiuza Ndi Zakhala Hero
Ine Mkumatsutsa Rest In Peace To My Daddy
Mukufunika Tsache Ndi Broom
Azam, U-fresh Ndi Boom
Tikumane Tikhale Nkati Mu
Ti Clean Hip Hop Nkatimu
Kapena Tiitane Mumba (Eeeh)
Kapena Tiitane Mumba (Iwee)
Kapena Tiitane Mumba (Eeeh)
Kapena Tiitane Mumba (Haha)
Related Songs –
Frequently Asked Questions
Who is the singer of the “Mumba” song?
The “Mumba” song is sung by Waxy Kay and Kinta.
Who wrote the lyrics to the “Mumba” song?
The song “Mumba” was written by Waxy Kay and Kinta.
Who is the music producer of the “Mumba” song?
“Mumba” is produced by [?].
When was the “Mumba“ song released?
Mumba was released on May 10, 2025.
What is the duration of Mumba?
The duration of the song Mumba is approximately 2 minutes and 24 seconds long.
This is the end of “Mumba Song Lyrics” by Waxy Kay and Kinta. Lyrics displayed here are for educational purposes only. We respect the artists and don’t promote copyright infringement instead. If you like this song please share it. If you find any mistakes in the lyrics or credits, please feel free to submit the correct version via the Contact Us section.